Tulani Madandaulo ena kudzera pa EthicsPoint™ |
Chitani Kalondolondo wa Dandaulo lomwe Munadzatula Kale |
|
Kupereka ku mabungwe njira zotulilapo madandaulo mwachinsinsi.
Cholinga cha kampani ya NAVEX ndi kuonetsetsa kuti inu mutha kuyankhulana nkhani ndi nkhawa zokhudza mchitidwe osayenera kapena osaloledwa pakati pa akuluakulu oyendetsa ntchito za bungwe kapena komiti yaikulu yoyang'anira ntchito za bungwe, ndi kuti mukutha kuyankhula zimenezi motetezeka komanso mwachilungamo popanda inu kudziwika kuti ndinu mwapanga zimenezi. Timayesetsa kuti ntchito yotula madandaulo kudzera pa EthicsPoint™ ikhale yosavuta komanso yosalira zambiri.. Masamba a paintaneti otsatirawa adzakuthandizani kutula madandaulo munjira yomwe inu simudzadziwika nkomwe. Tsatirani ndondomeko izi kuti mutule madandaulo anu:
Mukamaliza kutula dandaulo lanu, mudzapatsidwa nambala ya dandaulo yanu. Pasiwedi ndi nambala ya dandaulo yanu zidzakuthandizani kulondoloza za nkhani yomwe mwatulayi. |
|